Masalimo 2:6 - Buku Lopatulika6 Koma Ine ndadzoza mfumu yanga Pa Ziyoni, phiri langa loyera. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Koma Ine ndadzoza mfumu yanga Pa Ziyoni, phiri langa loyera. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Adzati, “Ine ndakhazika kale mfumu yanga, ili pa phiri langa loyera la Ziyoni.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 “Ine ndakhazikitsa mfumu yanga pa Ziyoni, phiri langa loyera.” Onani mutuwo |