Masalimo 2:5 - Buku Lopatulika5 Pomwepo adzalankhula nao mu mkwiyo wake, nadzawaopsa mu ukali wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Pomwepo adzalankhula nao mu mkwiyo wake, nadzawaopsa m'ukali wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Tsono adzaŵadzudzula ali wokwiya adzaŵaopseza ali wokalipa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Ndipo iye awadzudzula mu mkwiyo wake ndi kuwaopseza mu ukali wake, kunena kuti, Onani mutuwo |