Masalimo 148:3 - Buku Lopatulika3 Mlemekezeni, dzuwa ndi mwezi; mlemekezeni, nyenyezi zonse zounikira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Mlemekezeni, dzuwa ndi mwezi; mlemekezeni, nyenyezi zonse zounikira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Mtamandeni inu dzuŵa ndi mwezi, mtamandeni inu nonse nyenyezi zoŵala! Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Mutamandeni, inu dzuwa ndi mwezi, mutamandeni, inu nonse nyenyezi zowala. Onani mutuwo |