Masalimo 148:2 - Buku Lopatulika2 Mlemekezeni, angelo ake onse; mlemekezeni, makamu ake onse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Mlemekezeni, angelo ake onse; mlemekezeni, makamu ake onse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Mtamandeni inu angelo ake onse, mtamandeni inu magulu a ankhondo ake onse! Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Mutamandeni, inu angelo ake onse, mutamandeni, mutamandeni, inu zolengedwa za mmwamba. Onani mutuwo |