Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 148:1 - Buku Lopatulika

1 Aleluya. Lemekezani Yehova kochokera kumwamba; mlemekezeni m'misanje.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

1 Aleluya. Lemekezani Yehova kochokera kumwamba; mlemekezeni m'misanje.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

1 Tamandani Chauta! Tamandani Chauta inu okhala kumwamba, mtamandeni inu okhala mu mlengalenga!

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

1 Tamandani Yehova. Tamandani Yehova, inu a kumwamba, mutamandeni Iye, inu a mlengalenga.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 148:1
8 Mawu Ofanana  

Lemekezani Yehova, inu, ntchito zake zonse, ponseponse pali ufumu wake: Lemekeza Yehova, moyo wanga iwe.


Aleluya; Ulemekeze Yehova, moyo wanga.


Zakumwamba ndi dziko lapansi zimlemekeze, nyanja ndi zonse zoyenda m'mwemo.


Ndipo kumwamba kudzalemekeza zodabwitsa zanu, Yehova; chikhulupiriko chanunso mu msonkhano wa oyera mtima.


Imbani inu, m'mwamba, nukondwere iwe dziko lapansi, imbani inu mapiri, pakuti Yehova watonthoza mtima wa anthu ake, nadzachitira chifundo ovutidwa ake.


Ndipo mipingo yakumtsogolera ndi yakumtsatira, inafuula, kuti, Hosana kwa Mwana wa Davide! Wolemekezeka ndiye wakudza m'dzina la Ambuye! Hosana mu Kumwambamwamba!


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa