Masalimo 146:8 - Buku Lopatulika8 Yehova apenyetsa osaona; Yehova aongoletsa onse owerama; Yehova akonda olungama. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Yehova apenyetsa osaona; Yehova aongoletsa onse owerama; Yehova akonda olungama. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Chauta amatsekula maso a anthu osapenya, Chauta amakweza anthu otsitsidwa. Chauta amakonda anthu ochita chilungamo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Yehova amatsekula maso anthu osaona, Yehova amadzutsa onse amene awerama pansi, Yehova amakonda anthu olungama. Onani mutuwo |