Masalimo 146:7 - Buku Lopatulika7 ndiye wakuchitira chiweruzo osautsika; ndiye wakupatsa anjala chakudya; Yehova amasula akaidi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 ndiye wakuchitira chiweruzo osautsika; ndiye wakupatsa anjala chakudya; Yehova amasula akaidi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Amachitira anthu opsinjidwa zolungama, amaŵapatsa chakudya anthu anjala. Chauta amamasula am'ndende. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Iye amachitira chilungamo anthu oponderezedwa ndipo amapereka chakudya kwa anthu anjala. Yehova amamasula amʼndende, Onani mutuwo |