Masalimo 146:6 - Buku Lopatulika6 Amene analenga kumwamba ndi dziko lapansi, nyanja ndi zonse zili m'mwemo. Ndiye wakusunga choonadi kosatha, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Amene analenga zakumwamba ndi dziko lapansi, nyanja ndi zonse zili m'mwemo. Ndiye wakusunga choonadi kosatha, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Chauta adalenga kumwamba ndi dziko lapansi, nyanja ndi zonse zimene zili m'menemo. Amasunga malonjezo ake nthaŵi zonse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Wolenga kumwamba ndi dziko lapansi, nyanja ndi zonse zili mʼmenemo; Yehova, amene ndi wokhulupirika kwamuyaya. Onani mutuwo |