Masalimo 146:10 - Buku Lopatulika10 Yehova adzachita ufumu kosatha, Mulungu wako, Ziyoni, ku mibadwomibadwo. Aleluya. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Yehova adzachita ufumu kosatha, Mulungu wako, Ziyoni, ku mibadwomibadwo. Aleluya. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Chauta adzakhala mfumu mpaka muyaya, Mulungu wako, iwe Ziyoni, adzalamulira ku mibadwo yonse. Tamandani Chauta! Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Yehova ndiye Mfumu mpaka muyaya, Mulungu wako iwe Ziyoni, pa mibado yonse. Tamandani Yehova. Onani mutuwo |