Masalimo 147:1 - Buku Lopatulika1 Aleluya; Pakuti kuimbira zomlemekeza Mulungu wathu nkokoma; pakuti chikondweretsa ichi, chilemekezo chiyenera. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Aleluya; Pakuti kuimbira zomlemekeza Mulungu wathu nkokoma; pakuti chikondwetsa ichi, chilemekezo chiyenera. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Tamandani Chauta! Nkwabwino kuimba nyimbo zotamanda Mulungu wathu, nkokondwetsa mtima kumtamanda moyenera. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Tamandani Yehova. Nʼkwabwino kwambiri kuyimba nyimbo zamatamando kwa Mulungu wathu, nʼkokondweretsa ndi koyenera kumutamanda! Onani mutuwo |