Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 128:5 - Buku Lopatulika

5 Yehova adzakudalitsa ali mu Ziyoni; ndipo udzaona zokoma za Yerusalemu masiku onse a moyo wako.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Yehova adzakudalitsa ali m'Ziyoni; ndipo udzaona zokoma za Yerusalemu masiku onse a moyo wako.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Chauta amene amakhala ku Ziyoni akudalitse. Uwone m'mene Yerusalemu zinthu zidzamuyendere bwino masiku onse a moyo wako.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Yehova akudalitse kuchokera mʼZiyoni masiku onse a moyo wako; uwone zokoma za Yerusalemu,

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 128:5
9 Mawu Ofanana  

Wodala wakudzayo m'dzina la Yehova; takudalitsani kochokera m'nyumba ya Yehova.


Mupempherere mtendere wa Yerusalemu; akukonda inu adzaona phindu.


Yehova, ali mu Ziyoni, akudalitseni; ndiye amene analenga kumwamba ndi dziko lapansi.


Alemekezedwe Yehova kuchokera mu Ziyoni, amene akhala mu Yerusalemu. Aleluya.


likutumizire thandizo lotuluka m'malo oyera, ndipo likugwirizize kuchokera mu Ziyoni;


likumbukire zopereka zako zonse, lilandire nsembe yako yopsereza;


Ndipo anthu ambiri adzanka, nati, Tiyeni tikwere kunka kuphiri la Yehova, kunyumba ya Mulungu wa Yakobo; ndipo Iye adzatiphunzitsa za njira zake, ndipo tidzayenda m'mayendedwe ake; chifukwa mu Ziyoni mudzatuluka chilamulo, ndi mau a Yehova kuchokera mu Yerusalemu.


Tayang'ana pa Ziyoni, mzinda wa zikondwerero zathu; maso ako adzaona, Yerusalemu malo a phee, chihema chimene sichidzasunthidwa, zichiri zake sizidzazulidwa konse, zingwe zake sizidzadulidwa.


Wolemekezeka Mulungu ndi Atate wa Ambuye wathu Yesu Khristu, amene anatidalitsa ife ndi dalitso lonse la mzimu m'zakumwamba mwa Khristu;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa