Masalimo 128:6 - Buku Lopatulika6 Inde, udzaona zidzukulu zako. Mtendere ukhale ndi Israele. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Inde, udzaona zidzukulu zako. Mtendere ukhala ndi Israele. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Ukhale ndi moyo wautali kuti uwone zidzukulu zako. Mtendere ukhale ndi Israele. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 ndipo ukhale ndi moyo kuti udzaone zidzukulu zako. Mtendere ukhale ndi Israeli. Onani mutuwo |