Masalimo 128:4 - Buku Lopatulika4 Taonani, m'mwemo adzadalitsika munthu wakuopa Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Taonani, m'mwemo adzadalitsika munthu wakuopa Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Zoonadi, ndimo m'mene adzakhalire wodala munthu woopa Chauta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Ameneyu ndiye munthu wodalitsidwa amene amaopa Yehova. Onani mutuwo |