Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 114:3 - Buku Lopatulika

3 Nyanjayo inaona, nithawa; Yordani anabwerera m'mbuyo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Nyanjayo inaona, nithawa; Yordani anabwerera m'mbuyo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Nyanja idaona zimenezi nithaŵa, mtsinje wa Yordani udabwerera m'mbuyo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Nyanja inaona ndi kuthawa, mtsinje wa Yorodani unabwerera mʼmbuyo;

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 114:3
11 Mawu Ofanana  

Pa kudzudzula kwanu anathawa; anathawa msanga liu la bingu lanu;


Ndipo anadzudzula Nyanja Yofiira, ndipo inaphwa: Potero anawayendetsa mozama ngati m'chipululu.


Mudagawa kasupe ndi mtsinje; mudaphwetsa mitsinje yaikulu.


Madziwo anakuonani Mulungu; anakuonani madziwo; anachita mantha, zozama zomwe zinanjenjemera.


Makongwa anatsanula madzi; thambo lidamvetsa liu lake; mivi yanu yomwe inatulukira.


Ndipo Mose anatambasulira dzanja lake kunyanja; ndipo Yehova anabweza nyanja ndi mphepo yolimba ya kum'mawa usiku wonse, naumitsa nyanja; ndipo madziwo anagawikana.


Ndipo ndi mpumo wa m'mphuno mwanu madzi anaunjikika, mayendedwe ake anakhala chilili ngati mulu; zozama zinalimba m'kati mwa nyanja.


amene anayendetsa mkono wake waulemerero padzanja lamanja la Mose? Amene anagawanitsa madzi pamaso pao, kuti adzitengere mbiri yosatha?


Munaponda panyanja ndi akavalo anu, madzi amphamvu anaunjikana mulu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa