Masalimo 102:3 - Buku Lopatulika3 Popeza masiku anga akanganuka ngati utsi, ndi mafupa anga anyeka ngati nkhuni. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Popeza masiku anga akanganuka ngati utsi, ndi mafupa anga anyeka ngati nkhuni. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Masiku anga amangopita ngati utsi, ndipo thupi langa likuyaka ngati ng'anjo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Pakuti masiku anga akupita ngati utsi; mafupa anga akunyeka ngati nkhuni zoyaka. Onani mutuwo |