Masalimo 102:2 - Buku Lopatulika2 Musandibisire nkhope yanu tsiku la nsautso yanga; munditchereze khutu lanu; tsiku limene ndiitana ine mundiyankhe msanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Musandibisire nkhope yanu tsiku la nsautso yanga; munditchereze khutu lanu; tsiku limene ndiitana ine mundiyankhe msanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Musandibisire nkhope yanu pa tsiku la mavuto anga. Tcherani khutu kuti mundimve, mundiyankhe msanga pa tsiku limene ndikukuitanani. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Musandibisire nkhope yanu pamene ndili pa msautso. Munditcherere khutu; pamene ndiyitana ndiyankheni msanga. Onani mutuwo |