Masalimo 102:1 - Buku Lopatulika1 Yehova, imvani pemphero langa, ndipo mfuu wanga ufikire Inu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Yehova, imvani pemphero langa, ndipo mfuu wanga ufikire Inu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Inu Chauta, imvani pemphero langa, kulira kwanga kufike kwa Inu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Yehova imvani pemphero langa; kulira kwanga kopempha thandizo kufike kwa Inu. Onani mutuwo |