Masalimo 101:8 - Buku Lopatulika8 Mamawa onse ndidzadula oipa onse a m'dziko; kuduliratu onse akuchita zopanda pake kumzinda wa Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Mamawa onse ndidzadula oipa onse a m'dziko; kuduliratu onse akuchita zopanda pake kumudzi wa Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Tsiku ndi tsiku ndidzaononga oipa onse am'dziko. Onse ochita zoipa ndidzaŵachotsa mu mzinda wa Chauta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Mmawa uliwonse ndidzatontholetsa anthu onse oyipa mʼdziko; ndidzachotsa aliyense wochita zoyipa mu mzinda wa Yehova. Onani mutuwo |