Masalimo 101:7 - Buku Lopatulika7 Wakuchita chinyengo sadzakhala m'kati mwa nyumba yanga; wakunena mabodza sadzakhazikika pamaso panga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Wakuchita chinyengo sadzakhala m'kati mwa nyumba yanga; wakunena mabodza sadzakhazikika pamaso panga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Palibe munthu wochita zonyenga amene adzakhale m'nyumba mwanga. Palibe munthu wolankhula zabodza amene adzakhale pafupi ndi ine. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Aliyense wochita chinyengo sadzakhala mʼnyumba mwanga. Aliyense woyankhula mwachinyengo sadzayima pamaso panga. Onani mutuwo |