Masalimo 101:3 - Buku Lopatulika3 Sindidzaika chinthu choipa pamaso panga; chochita iwo akupatuka padera chindiipira; sichidzandimamatira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Sindidzaika chinthu choipa pamaso panga; chochita iwo akupatuka padera chindiipira; sichidzandimamatira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Sindidzaika maso anga pa chinthu chilichonse chachabechabe. Ndimadana ndi zochita za anthu okusiyani, sizindikomera konse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Sindidzayika chinthu chilichonse choyipa pamaso panga. Ine ndimadana ndi zochita za anthu opanda chikhulupiriro; iwo sadzadziphatika kwa ine. Onani mutuwo |