Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 101:4 - Buku Lopatulika

4 Mtima wopulukira udzandichokera; sindidzadziwana naye woipa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 Mtima wopulukira udzandichokera; sindidzadziwana naye woipa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 Ndidzakhala kutali ndi anthu a mtima woipa, sindidzalola choipa chilichonse kuloŵa mwa ine.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Anthu a mtima wokhota adzakhala kutali ndi ine; ine sindidzalola choyipa chilichonse kulowa mwa ine.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 101:4
15 Mawu Ofanana  

Mundichokere ochita zoipa inu; kuti ndisunge malamulo a Mulungu wanga.


Sindinakhala pansi ndi anthu achabe; kapena kutsagana nao anthu othyasika.


Ndidana nao msonkhano wa ochimwa, ndipo sindidzakhala nao pansi ochita zoipa.


Chokani kwa ine, nonsenu akuchita zopanda pake; pakuti wamva Yehova mau a kulira kwanga.


Okhota mtima anyansa Yehova; koma angwiro m'njira zao amsekeretsa.


Usayanjane ndi munthu wokwiya msanga; ngakhale kupita ndi mwamuna waukali;


Munthu woipa anyansa olungama; ndipo woongoka m'njira anyansa wochimwa.


Pakuti wamphulupulu anyansa Yehova; koma chinsinsi chake chili ndi oongoka.


Kuopa Yehova ndiko kuda zoipa; kunyada, ndi kudzikuza, ndi njira yoipa, ndi m'kamwa mokhota, ndizida.


Lekani, achibwana inu, nimukhale ndi moyo; nimuyende m'njira ya nzeru.


Ndipo pamenepo ndidzafukulira iwo, Sindinakudziweni inu nthawi zonse; chokani kwa Ine, inu akuchita kusaweruzika.


ndipo mwa zenera, mudengu, ananditsitsa pakhoma, ndipo ndinapulumuka m'manja mwake.


Koma ndithu maziko a Mulungu aimika pokhazikika, ndi kukhala nacho chizindikiro ichi, Ambuye azindikira iwo amene ali ake; ndipo, Adzipatule kwa chosalungama yense wakutchula dzina la Ambuye.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa