Masalimo 1:4 - Buku Lopatulika4 Oipa satero ai; koma akunga mungu wouluka ndi mphepo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Oipa satero ai; koma akunga mungu wouluka ndi mphepo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Anthu oipa sali choncho, ali ngati mungu wouluzika ndi mphepo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Sizitero ndi anthu oyipa! Iwo ali ngati mungu umene umawuluzidwa ndi mphepo. Onani mutuwo |