Yohane 3:1 - Buku Lopatulika Koma panali munthu wa Afarisi, dzina lake Nikodemo, mkulu wa Ayuda. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Koma panali munthu wa Afarisi, dzina lake Nikodemo, mkulu wa Ayuda. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Munthu wina wa m'gulu la Afarisi, dzina lake Nikodemo, mkulu wa Ayuda, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ndipo panali Mfarisi wotchedwa Nekodimo, wa mʼgulu lolamulira la Ayuda. |
Koma anadzanso Nikodemo, amene anadza kwa Iye usiku poyamba paja, alikutenga chisakanizo cha mure ndi aloe, monga miyeso zana.
Ndipo taona amalankhula poyera, ndipo sanena kanthu kwa Iye. Kapena kodi akulu adziwa ndithu kuti ndiye Khristu ameneyo?