Yohane 3:10 - Buku Lopatulika10 Yesu anayankha nati kwa iye, Kodi uli mphunzitsi wa Israele, ndipo sudziwa izi? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Yesu anayankha nati kwa iye, Kodi uli mphunzitsi wa Israele, ndipo sudziwa izi? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Yesu adati, “Kodi iwe sindiwe mphunzitsi wodziŵika pakati pa Aisraele, nanga sukumvetsa bwanji zimenezi? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Yesu anati, “Iwe mphunzitsi wa Israeli, kodi sukuzindikira zimenezi? Onani mutuwo |