Tsopano mwalamulidwa chitani ichi; muwatengere ana anu ndi akazi magaleta a m'dziko la Ejipito; nimubwere naye atate wanu.
Numeri 7:6 - Buku Lopatulika Ndipo Mose analandira magaleta ndi ng'ombe, nazipereka kwa Alevi. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Mose analandira magaleta ndi ng'ombe, nazipereka kwa Alevi. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Choncho Mose adatenga ngolo ndi ng'ombe zija nazipereka kwa Alevi. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Choncho Mose anatenga ngolo ndi ngʼombe zothenazo nazipereka kwa Alevi. |
Tsopano mwalamulidwa chitani ichi; muwatengere ana anu ndi akazi magaleta a m'dziko la Ejipito; nimubwere naye atate wanu.
Ndipo anagwetsa chihema; ndi ana a Geresoni, ndi ana a Merari, akunyamula chihema, anamuka nacho.
Uzilandira kwa iwo, kuti zikhale zakuchitira ntchito ya chihema chokomanako; nuzipereke kwa Alevi, yense monga mwa ntchito yake.