Numeri 7:7 - Buku Lopatulika7 Anapatsa ana a Geresoni magaleta awiri ndi ng'ombe zinai, monga mwa ntchito yao; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Anapatsa ana a Geresoni magaleta awiri ndi ng'ombe zinai, monga mwa ntchito yao; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Ana a Geresoni adaŵapatsa ngolo ziŵiri ndi ng'ombe zinai potsata ntchito yao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Anapereka ngolo ziwiri ndi ngʼombe zothena zinayi kwa Ageresoni monga mwantchito yawo Onani mutuwo |