Numeri 7:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo Mose analandira magaleta ndi ng'ombe, nazipereka kwa Alevi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo Mose analandira magaleta ndi ng'ombe, nazipereka kwa Alevi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Choncho Mose adatenga ngolo ndi ng'ombe zija nazipereka kwa Alevi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Choncho Mose anatenga ngolo ndi ngʼombe zothenazo nazipereka kwa Alevi. Onani mutuwo |