Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 7:5 - Buku Lopatulika

5 Uzilandira kwa iwo, kuti zikhale zakuchitira ntchito ya chihema chokomanako; nuzipereke kwa Alevi, yense monga mwa ntchito yake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Uzilandira kwa iwo, kuti zikhale zakuchitira ntchito ya chihema chokomanako; nuzipereke kwa Alevi, yense monga mwa ntchito yake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 “Ulandire zimenezi kwa anthuwo kuti zithandize potumikira m'chihema chamsonkhano. Uŵapatse Alevi zimenezo, aliyense zoyenera ntchito yake.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 “Ulandire zimenezi kwa iwo kuti zigwire ntchito ku tenti ya msonkhano. Uzipereke kwa Alevi, aliyense monga mwa ntchito yake.”

Onani mutuwo Koperani




Numeri 7:5
9 Mawu Ofanana  

Ndipo Yehova ananena ndi Mose, ndi kuti,


Ndipo Mose analandira magaleta ndi ng'ombe, nazipereka kwa Alevi.


Okhulupirika mauwa, ndipo za izi ndifuna kuti ulimbitse mau, kuti iwo akukhulupirira Mulungu asamalire akhalebe atsogoleri a ntchito zabwino. Izi nzokoma ndi zopindulitsa anthu;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa