Numeri 7:5 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 “Ulandire zimenezi kwa iwo kuti zigwire ntchito ku tenti ya msonkhano. Uzipereke kwa Alevi, aliyense monga mwa ntchito yake.” Onani mutuwoBuku Lopatulika5 Uzilandira kwa iwo, kuti zikhale zakuchitira ntchito ya chihema chokomanako; nuzipereke kwa Alevi, yense monga mwa ntchito yake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Uzilandira kwa iwo, kuti zikhale zakuchitira ntchito ya chihema chokomanako; nuzipereke kwa Alevi, yense monga mwa ntchito yake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 “Ulandire zimenezi kwa anthuwo kuti zithandize potumikira m'chihema chamsonkhano. Uŵapatse Alevi zimenezo, aliyense zoyenera ntchito yake.” Onani mutuwo |