Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 7:6 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Choncho Mose anatenga ngolo ndi ngʼombe zothenazo nazipereka kwa Alevi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

6 Ndipo Mose analandira magaleta ndi ng'ombe, nazipereka kwa Alevi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Ndipo Mose analandira magaleta ndi ng'ombe, nazipereka kwa Alevi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Choncho Mose adatenga ngolo ndi ng'ombe zija nazipereka kwa Alevi.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 7:6
4 Mawu Ofanana  

“Uwawuzenso kuti, ‘Tengani ngolo zingapo za kuno ku Igupto kuti mukakwezepo ana anu, akazi anu pamodzi ndi abambo ako ndi kubwera nawo kuno.


Kenaka anagwetsa chihema, ndipo Ageresoni ndi Amerari amene ananyamula chihemacho, ananyamuka.


“Ulandire zimenezi kwa iwo kuti zigwire ntchito ku tenti ya msonkhano. Uzipereke kwa Alevi, aliyense monga mwa ntchito yake.”


Anapereka ngolo ziwiri ndi ngʼombe zothena zinayi kwa Ageresoni monga mwantchito yawo


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa