Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 7:7 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 Anapereka ngolo ziwiri ndi ngʼombe zothena zinayi kwa Ageresoni monga mwantchito yawo

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

7 Anapatsa ana a Geresoni magaleta awiri ndi ng'ombe zinai, monga mwa ntchito yao;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 Anapatsa ana a Geresoni magaleta awiri ndi ng'ombe zinai, monga mwa ntchito yao;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Ana a Geresoni adaŵapatsa ngolo ziŵiri ndi ng'ombe zinai potsata ntchito yao.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 7:7
4 Mawu Ofanana  

“Uwawuzenso kuti, ‘Tengani ngolo zingapo za kuno ku Igupto kuti mukakwezepo ana anu, akazi anu pamodzi ndi abambo ako ndi kubwera nawo kuno.


Choncho Mose anatenga ngolo ndi ngʼombe zothenazo nazipereka kwa Alevi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa