Genesis 45:19 - Buku Lopatulika19 Tsopano mwalamulidwa chitani ichi; muwatengere ana anu ndi akazi magaleta a m'dziko la Ejipito; nimubwere naye atate wanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Tsopano mwalamulidwa chitani ichi; muwatengere ana anu ndi akazi magaleta a m'dziko la Ejipito; nimubwere naye atate wanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Uŵauze kuti atenge ngolo za kuno ku Ejipito, kuti akazi ao akakwerepo pamodzi ndi ana omwe. Ndithu akamtenge bambo wao akabwere kuno. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 “Uwawuzenso kuti, ‘Tengani ngolo zingapo za kuno ku Igupto kuti mukakwezepo ana anu, akazi anu pamodzi ndi abambo ako ndi kubwera nawo kuno. Onani mutuwo |