Numeri 4:22 - Buku Lopatulika Werenganso ana a Geresoni, monga mwa nyumba za makolo ao, monga mwa mabanja ao. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Werenganso ana a Geresoni, monga mwa nyumba za makolo ao, monga mwa mabanja ao. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa “Uŵerengenso ana a Geresoni potsata mabanja ao ndiponso banja la makolo ao. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero “Werenganso Ageresoni monga mwa mabanja ndi mafuko awo. |
Uwawerenge kuyambira a zaka makumi atatu ndi mphambu, kufikira a zaka makumi asanu; onse akulowa kutumikira utumikiwo, kuchita ntchitoyi m'chihema chokomanako.