Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 3:24 - Buku Lopatulika

24 Ndipo kalonga wa nyumba ya makolo a Ageresoni ndiye Eliyasafu mwana wa Laele.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

24 Ndipo kalonga wa nyumba ya makolo a Ageresoni ndiye Eliyasafu mwana wa Laele.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

24 Eliyasafu mwana wa Laele ndiye anali mtsogoleri wa banja la makolo a Ageresoni.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

24 Mtsogoleri wa mabanja a Ageresoni anali Eliyasafu mwana wa Laeli.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 3:24
3 Mawu Ofanana  

Mabanja a Ageresoni azimanga mahema ao pambuyo pa chihema kumadzulo.


Ndipo udikiro wa ana a Geresoni m'chihema, chokomanako ndiwo Kachisi, ndi chihema, chophimba chake, ndi nsalu yotsekera pa khomo la chihema chokomanako,


Werenganso ana a Geresoni, monga mwa nyumba za makolo ao, monga mwa mabanja ao.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa