Ndipo anayenda kuchokera kuphiri la Yehova ulendo wa masiku atatu; ndipo likasa la chipangano cha Yehova, linawatsogolera ulendo wa masiku atatu kuwafunira popumulira.
Numeri 33:16 - Buku Lopatulika Nachokera ku chipululu cha Sinai, nayenda namanga mu Kibroti-Hatava. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Nachokera ku chipululu cha Sinai, nayenda namanga m'Kibroti-Hatava. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Adanyamuka ku chipululu cha Sinai, nakamanga mahema ao ku Kibroti-Hatava. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Atachoka ku chipululu cha Sinai anakamanga misasa yawo ku Kiburoti-Hataava. |
Ndipo anayenda kuchokera kuphiri la Yehova ulendo wa masiku atatu; ndipo likasa la chipangano cha Yehova, linawatsogolera ulendo wa masiku atatu kuwafunira popumulira.
Ndipo anthu osokonezeka ali pakati pao anagwidwa nacho chilakolako; ndi ana a Israele omwe analiranso, nati, Adzatipatsa nyama ndani?
Yehova Mulungu wathu ananena ndi ife mu Horebu, ndi kuti Yakwanira nthawi yokhala inu m'phiri muno;