Numeri 33:17 - Buku Lopatulika17 Nachokera ku Kibroti-Hatava, nayenda namanga mu Hazeroti. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Nachokera ku Kibroti-Hatava, nayenda namanga m'Hazeroti. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Adanyamuka ku Kibroti-Hatava, nakamanga mahema ao ku Haseroti. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Atachoka ku Kiburoti-Hataava anakamanga misasa yawo ku Heziroti. Onani mutuwo |