Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 33:16 - Buku Lopatulika

16 Nachokera ku chipululu cha Sinai, nayenda namanga mu Kibroti-Hatava.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

16 Nachokera ku chipululu cha Sinai, nayenda namanga m'Kibroti-Hatava.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

16 Adanyamuka ku chipululu cha Sinai, nakamanga mahema ao ku Kibroti-Hatava.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

16 Atachoka ku chipululu cha Sinai anakamanga misasa yawo ku Kiburoti-Hataava.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 33:16
6 Mawu Ofanana  

Ndipo anayenda kuchokera kuphiri la Yehova ulendo wa masiku atatu; ndipo likasa la chipangano cha Yehova, linawatsogolera ulendo wa masiku atatu kuwafunira popumulira.


Ndipo anatcha malowo dzina lake Kibroti-Hatava; popeza pamenepo anaika anthu osusuka.


Ndipo anthu osokonezeka ali pakati pao anagwidwa nacho chilakolako; ndi ana a Israele omwe analiranso, nati, Adzatipatsa nyama ndani?


Nachokera ku Kibroti-Hatava, nayenda namanga mu Hazeroti.


Yehova Mulungu wathu ananena ndi ife mu Horebu, ndi kuti Yakwanira nthawi yokhala inu m'phiri muno;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa