Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 33:15 - Buku Lopatulika

15 Ndipo anachokera ku Refidimu, nayenda namanga m'chipululu cha Sinai.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

15 Ndipo anachokera ku Refidimu, nayenda namanga m'chipululu cha Sinai.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

15 Adanyamuka ku Refidimu, nakamanga mahema ao ku chipululu cha Sinai.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

15 Atachoka ku Refidimu anakamanga ku chipululu cha Sinai

Onani mutuwo Koperani




Numeri 33:15
3 Mawu Ofanana  

Ndipo anachoka ku Elimu, ndi khamu lonse la ana a Israele linalowa m'chipululu cha Sini, ndicho pakati pa Elimu ndi Sinai, tsiku lakhumi ndi chisanu la mwezi wachiwiri atatuluka m'dziko la Ejipito.


Ndipo ana a Israele anayenda monga mwa maulendo ao, kuchokera m'chipululu cha Sinai; ndi mtambo unakhala m'chipululu cha Parani.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa