Numeri 33:14 - Buku Lopatulika14 Nachokera ku Alusi, nayenda namanga mu Refidimu; kumeneko kunalibe madzi kuti anthu amwe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Nachokera ku Alusi, nayenda namanga m'Refidimu; kumeneko kunalibe madzi kuti anthu amwe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Adanyamuka ku Alusi, nakamanga mahema ao ku Refidimu kumene kunalibe madzi akumwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Atachoka ku Alusi anakamanga misasa yawo ku Refidimu, kumene kunalibe madzi woti anthu ndi kumwa. Onani mutuwo |