Numeri 33:13 - Buku Lopatulika13 Nachokera ku Dofika, nayenda namanga mu Alusi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Nachokera ku Dofika, nayenda namanga m'Alusi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Adanyamuka ku Dofika, nakamanga mahema ao ku Alusi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Atachoka ku Dofika anakamanga misasa yawo ku Alusi. Onani mutuwo |