Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 33:12 - Buku Lopatulika

12 Nachokera ku chipululu cha Sini, nayenda namanga mu Dofika.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Nachokera ku chipululu cha Sini, nayenda namanga m'Dofika.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 Adanyamuka ku chipululu cha Sini, nakamanga mahema ao ku Dofika.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 Atachoka ku chipululu cha Sini anakamanga ku Dofika.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 33:12
3 Mawu Ofanana  

Ndipo khamu lonse la ana a Israele linachoka m'chipululu cha Sini, M'zigono zao, monga mwa mau a Yehova, nagona mu Refidimu. Koma kumeneko kunalibe madzi akumwa anthu.


Nachokera ku Nyanja Yofiira, nayenda namanga m'chipululu cha Sini.


Nachokera ku Dofika, nayenda namanga mu Alusi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa