Numeri 33:11 - Buku Lopatulika11 Nachokera ku Nyanja Yofiira, nayenda namanga m'chipululu cha Sini. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Nachokera ku Nyanja Yofiira, nayenda namanga m'chipululu cha Sini. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Adanyamuka ku Nyanja Yofiira, nakamanga mahema ao ku chipululu cha Sini. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Atachoka ku Nyanja Yofiira anakamanga misasa yawo mʼchipululu cha Sini. Onani mutuwo |