Numeri 33:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo anachokera ku Elimu, nayenda namanga ku Nyanja Yofiira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo anachokera ku Elimu, nayenda namanga ku Nyanja Yofiira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Adanyamuka ku Elimu, nakamanga mahema ao m'mbali mwa Nyanja Yofiira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Atachoka ku Elimu anakamanga misasa yawo mʼmbali mwa Nyanja Yofiira. Onani mutuwo |