Numeri 33:18 - Buku Lopatulika18 Nachokera ku Hazeroti, nayenda namanga mu Ritima. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Nachokera ku Hazeroti, nayenda namanga m'Ritima. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Adanyamuka ku Hazeroti, nakamanga mahema ao ku Ritima. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Atachoka ku Heziroti anakamanga ku Ritima. Onani mutuwo |