Numeri 33:19 - Buku Lopatulika19 Nachokera ku Ritima, nayenda namanga mu Rimoni-Perezi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Nachokera ku Ritima, nayenda namanga m'Rimoni-Perezi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Adanyamuka ku Ritima, nakamanga mahema ao ku Rimoni-Perezi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Atachoka ku Ritima anakamanga ku Rimoni-Perezi. Onani mutuwo |