Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 33:20 - Buku Lopatulika

20 Nachokera ku Rimoni-Perezi, nayenda namanga mu Libina.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

20 Nachokera ku Rimoni-Perezi, nayenda namanga m'Libina.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

20 Adanyamuka ku Rimoni-Perezi, nakamanga mahema ao ku Libina.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

20 Atachoka ku Rimoni-Perezi anakamanga ku Libina.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 33:20
6 Mawu Ofanana  

Ndipo kazembeyo anabwerera, napeza mfumu ya Asiriya ilikuponyana nkhondo ndi Libina; pakuti anamva kuti inachoka ku Lakisi.


Ndipo Mose anawatuma a fuko limodzi chikwi chimodzi, kunkhondo, iwowa ndi Finehasi mwana wa Eleazara wansembe, kunkhondo, ndi zipangizo zopatulika, ndi malipenga oliza m'dzanja lake.


Nachokera ku Ritima, nayenda namanga mu Rimoni-Perezi.


Nachokera ku Libina, nayenda namanga mu Risa.


Awa ndi mau amene Mose ananena kwa Israele wonse, tsidya la Yordani m'chipululu, m'chidikha cha pandunji pa Sufu, pakati pa Parani, ndi Tofele, ndi Labani, ndi Hazeroti, ndi Dizahabu.


Pamenepo Yoswa ndi Aisraele onse naye anapitirira kuchokera ku Makeda kunka ku Libina, nathira nkhondo pa Libina;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa