Numeri 11:34 - Buku Lopatulika34 Ndipo anatcha malowo dzina lake Kibroti-Hatava; popeza pamenepo anaika anthu osusuka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 Ndipo anatcha malowo dzina lake Kibroti-Hatava; popeza pamenepo anaika anthu osusuka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa34 Nchifukwa chake malowo adaŵatcha Mandaankhuli, chifukwa choti kumeneko ndiko kumene adakwirira anthu ankhuli. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 Nʼchifukwa chake malowo anawatcha Kibiroti Hatava chifukwa pamenepo anakwirirapo anthu osusuka aja. Onani mutuwo |