Numeri 11:35 - Buku Lopatulika35 Kuchokera ku Kibroti-Hatava anthuwo anayenda kunka ku Hazeroti; nakhala ku Hazeroti. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201435 Kuchokera ku Kibroti-Hatava anthuwo anayenda kunka ku Hazeroti; nakhala ku Hazeroti. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa35 Kuchokera ku Mandaankhuliko, anthu adapita ku Hazeroti, ndipo adakhala komweko. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero35 Kuchoka pa Kibiroti Hatava anthuwo anayenda kupita ku Heziroti ndipo anakhala kumeneko kwa kanthawi. Onani mutuwo |