Numeri 2:14 - Buku Lopatulika Ndi fuko la Gadi; kalonga wa ana a Gadi ndiye Eliyasafu mwana wa Reuwele. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndi fuko la Gadi; kalonga wa ana a Gadi ndiye Eliyasafu mwana wa Reuwele. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Tsono pabwere fuko la Gadi, limene mtsogoleri wake ndi Eliyasafu, mwana wa Deuwele, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Lotsatira lidzakhala fuko la Gadi. Mtsogoleri wa gulu la Gadi ndi Eliyasafu mwana wa Deuweli. |
Ndi khamu lake ndi owerengedwa ake, ndiwo zikwi makumi asanu mphambu zisanu ndi zinai kudza mazana atatu.
Ndi khamu lake, ndi owerengedwa ake, ndiwo zikwi makumi anai mphambu zisanu kudza mazana asanu ndi limodzi mphambu makumi asanu.
ndi nsembe yoyamika, ng'ombe ziwiri, nkhosa zamphongo zisanu, atonde asanu, anaankhosa asanu a chaka chimodzi; ndicho chopereka cha Eliyasafu mwana wa Deuwele.