Numeri 7:42 - Buku Lopatulika42 Tsiku lachisanu ndi chimodzi kalonga wa ana a Gadi, Eliyasafu mwana wa Deuwele: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201442 Tsiku lachisanu ndi chimodzi kalonga wa ana a Gadi, Eliyasafu mwana wa Deuwele: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa42 Tsiku lachisanu ndi chimodzi linali la Eliyasafu mwana wa Deuwele mtsogoleri wa Agadi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero42 Pa tsiku lachisanu ndi chimodzi, Eliyasafu mwana wa Deuweli, mtsogoleri wa fuko la Gadi, anabweretsa chopereka chake. Onani mutuwo |